Oweruza 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anati: “Pajatu ku Silo+ kumachitika chikondwerero cha Yehova chaka chilichonse. Mzinda wa Silo uli kumpoto kwa Beteli, chakumʼmawa kwa msewu waukulu wochokera ku Beteli kupita ku Sekemu, ndiponso kumʼmwera kwa Lebona.”
19 Kenako anati: “Pajatu ku Silo+ kumachitika chikondwerero cha Yehova chaka chilichonse. Mzinda wa Silo uli kumpoto kwa Beteli, chakumʼmawa kwa msewu waukulu wochokera ku Beteli kupita ku Sekemu, ndiponso kumʼmwera kwa Lebona.”