-
Oweruza 21:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Aisiraeli anayamba kubalalika kuchoka kumeneko ndipo aliyense anapita ku fuko lake ndi ku banja lake. Iwo anachoka kumeneko moti aliyense anapita ku cholowa chake.
-