Rute 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Naomi anauza apongozi akewo kuti: “Basi bwererani, aliyense apite kunyumba kwa amayi ake. Yehova akusonyezeni chikondi chokhulupirika+ ngati mmenenso inuyo munasonyezera chikondichi kwa amuna anu amene anamwalira ndiponso kwa ine. Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:8 Tsanzirani, ptsa. 36-37 Nsanja ya Olonda,7/1/2012, tsa. 253/1/2005, ptsa. 26-27
8 Naomi anauza apongozi akewo kuti: “Basi bwererani, aliyense apite kunyumba kwa amayi ake. Yehova akusonyezeni chikondi chokhulupirika+ ngati mmenenso inuyo munasonyezera chikondichi kwa amuna anu amene anamwalira ndiponso kwa ine.