-
Rute 1:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Atatero iwo analiranso mokweza. Kenako Olipa anakisa apongozi akewo nʼkubwerera. Koma Rute sanalole kusiyana nawo.