Rute 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Rute mkazi wa ku Mowabu uja anauza Naomi kuti: “Bwanji ndipite ndikakunkhe+ balere mʼmunda wa aliyense amene angandikomere mtima?” Ndipo Naomi anamuyankha kuti: “Pita mwana wanga.” Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Tsanzirani, ptsa. 39-40 Nsanja ya Olonda,7/1/2012, ptsa. 27-283/1/2005, tsa. 27
2 Rute mkazi wa ku Mowabu uja anauza Naomi kuti: “Bwanji ndipite ndikakunkhe+ balere mʼmunda wa aliyense amene angandikomere mtima?” Ndipo Naomi anamuyankha kuti: “Pita mwana wanga.”