Rute 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atafika anapempha kuti, ‘Ndimati ndikunkhe nawo.+ Ndizitola balere* wotsala pambuyo pa anthu amene akukololawa.’ Ndipo wakhala akukunkha kuyambira mʼmawa mpaka posachedwapa pamene anakhala pamthunzi kuti apume pangʼono.” Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2145 Nsanja ya Olonda,3/1/2005, tsa. 27
7 Atafika anapempha kuti, ‘Ndimati ndikunkhe nawo.+ Ndizitola balere* wotsala pambuyo pa anthu amene akukololawa.’ Ndipo wakhala akukunkha kuyambira mʼmawa mpaka posachedwapa pamene anakhala pamthunzi kuti apume pangʼono.”