Rute 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Boazi anamuyankha kuti: “Ndamva zonse zimene wachitira apongozi ako kuchokera pamene mwamuna wako anamwalira. Ndamvanso kuti unasiya bambo ako ndi mayi ako komanso dziko lakwanu, nʼkubwera kuno kwa anthu osawadziwa.+ Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Tsanzirani, tsa. 41 Nsanja ya Olonda,7/1/2012, tsa. 28
11 Boazi anamuyankha kuti: “Ndamva zonse zimene wachitira apongozi ako kuchokera pamene mwamuna wako anamwalira. Ndamvanso kuti unasiya bambo ako ndi mayi ako komanso dziko lakwanu, nʼkubwera kuno kwa anthu osawadziwa.+