-
Rute 3:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho samba nʼkudzola mafuta komanso utchene ndipo upite kumalo opunthirawo. Koma ukaonetsetse kuti iye asakadziwe kuti wafika mpaka atamaliza kudya ndi kumwa.
-