-
Rute 3:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Boazi anadya ndi kumwa ndipo anali wosangalala kwambiri. Kenako anapita kukagona kumapeto kwa mulu wa balere. Ndiyeno Rute anayenda mwakachetechete ndipo anavundukula mapazi a Boazi nʼkugona.
-