Rute 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho anafunsa kuti: “Ndiwe ndani?” Rute anayankha kuti: “Ndine Rute kapolo wanu. Ndifunditseni chovala chanu ine kapolo wanu, chifukwa ndinu wotiwombola.”+ Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Tsanzirani, tsa. 47 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, tsa. 224/15/2003, tsa. 25
9 Choncho anafunsa kuti: “Ndiwe ndani?” Rute anayankha kuti: “Ndine Rute kapolo wanu. Ndifunditseni chovala chanu ine kapolo wanu, chifukwa ndinu wotiwombola.”+