Rute 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atatero, Boazi anati: “Yehova akudalitse mwana wanga. Chikondi chokhulupirika chimene wasonyeza panopa chikuposa choyamba chija,+ chifukwa sunafune anyamata, kaya osauka kapena olemera. Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:10 Tsanzirani, tsa. 47 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, tsa. 22
10 Atatero, Boazi anati: “Yehova akudalitse mwana wanga. Chikondi chokhulupirika chimene wasonyeza panopa chikuposa choyamba chija,+ chifukwa sunafune anyamata, kaya osauka kapena olemera.