Rute 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gona pompano lero. Ngati iye angakuwombole mawa, zili bwino akuwombole.+ Koma ngati sakufuna kukuwombola, ineyo ndikuwombola. Ndithudi, pali Yehova Mulungu wamoyo, ndikuwombola. Gona mpaka mʼmawa.” Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Tsanzirani, tsa. 48 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, ptsa. 22-23
13 Gona pompano lero. Ngati iye angakuwombole mawa, zili bwino akuwombole.+ Koma ngati sakufuna kukuwombola, ineyo ndikuwombola. Ndithudi, pali Yehova Mulungu wamoyo, ndikuwombola. Gona mpaka mʼmawa.”