Rute 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zitatero, Boazi anapita kugeti la mzinda+ nʼkukhala pansi. Ali kumeneko anaona wowombola anamutchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe uje, tabwera udzakhale apa.” Choncho anapita nʼkukakhala pansi. Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Tsanzirani, tsa. 50 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, tsa. 24
4 Zitatero, Boazi anapita kugeti la mzinda+ nʼkukhala pansi. Ali kumeneko anaona wowombola anamutchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe uje, tabwera udzakhale apa.” Choncho anapita nʼkukakhala pansi.