Rute 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Boazi anauza wowombola uja+ kuti: “Naomi amene wabwerera kuchokera kudziko la Mowabu+ ayenera kugulitsa malo amene anali a mchimwene wathu Elimeleki.+
3 Ndiyeno Boazi anauza wowombola uja+ kuti: “Naomi amene wabwerera kuchokera kudziko la Mowabu+ ayenera kugulitsa malo amene anali a mchimwene wathu Elimeleki.+