Rute 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Boazi anauza akulu ndi anthu onse kuti: “Inu ndinu mboni+ lero kuti ndikugula kwa Naomi zinthu zonse zimene zinali za Elimeleki ndiponso zonse zimene zinali za Kiliyoni ndi Maloni. Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:9 Tsanzirani, tsa. 50 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, tsa. 24
9 Kenako Boazi anauza akulu ndi anthu onse kuti: “Inu ndinu mboni+ lero kuti ndikugula kwa Naomi zinthu zonse zimene zinali za Elimeleki ndiponso zonse zimene zinali za Kiliyoni ndi Maloni.