1 Samueli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsiku lina pamene Elikana ankapereka nsembe, anatenga magawo a nsembeyo nʼkupereka kwa mkazi wake Penina komanso ana ake onse aamuna ndi aakazi.+
4 Tsiku lina pamene Elikana ankapereka nsembe, anatenga magawo a nsembeyo nʼkupereka kwa mkazi wake Penina komanso ana ake onse aamuna ndi aakazi.+