1 Samueli 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hana anali wokhumudwa kwambiri ndipo anayamba kupemphera kwa Yehova+ uku akulira kwambiri.