1 Samueli 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zitatero Eli anamuyankha kuti: “Pita mumtendere, ndipo Mulungu wa Isiraeli akupatse zimene wamupempha.”+
17 Zitatero Eli anamuyankha kuti: “Pita mumtendere, ndipo Mulungu wa Isiraeli akupatse zimene wamupempha.”+