1 Samueli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Odya bwino ayenera kugwira ganyu kuti apeze chakudya,Koma anjala alibenso njala.+ Wosabereka wabereka ana 7,+Koma amene anali ndi ana aamuna ambiri, ali yekhayekha.*
5 Odya bwino ayenera kugwira ganyu kuti apeze chakudya,Koma anjala alibenso njala.+ Wosabereka wabereka ana 7,+Koma amene anali ndi ana aamuna ambiri, ali yekhayekha.*