1 Samueli 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Elikana anapita kunyumba kwake ku Rama, koma mwanayo anatsala nʼkumatumikira Yehova+ moyangʼaniridwa ndi wansembe Eli.
11 Kenako Elikana anapita kunyumba kwake ku Rama, koma mwanayo anatsala nʼkumatumikira Yehova+ moyangʼaniridwa ndi wansembe Eli.