1 Samueli 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu aliyense akamapereka nsembe ankayeneranso kupereka gawo la nyamayo kwa wansembe.+ Ndiyeno zimene zinkachitika nʼzakuti nyamayo ikamawira, mtumiki wa wansembe ankabwera foloko ya mano atatu ili mʼmanja.
13 Munthu aliyense akamapereka nsembe ankayeneranso kupereka gawo la nyamayo kwa wansembe.+ Ndiyeno zimene zinkachitika nʼzakuti nyamayo ikamawira, mtumiki wa wansembe ankabwera foloko ya mano atatu ili mʼmanja.