1 Samueli 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso chaka chilichonse amayi ake ankamusokera kamkanjo kodula manja. Iwo ankamupititsira kamalayako akapita ndi amuna awo kukapereka nsembe yapachaka.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Tsanzirani, ptsa. 57-58 Nsanja ya Olonda,7/1/2010, tsa. 18
19 Komanso chaka chilichonse amayi ake ankamusokera kamkanjo kodula manja. Iwo ankamupititsira kamalayako akapita ndi amuna awo kukapereka nsembe yapachaka.+