1 Samueli 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anakomera mtima Hana moti anabereka ana ena.+ Anabereka ana aamuna atatu ndi aakazi awiri. Ndipo Samueli anapitiriza kukula akutumikira Yehova.*+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:21 Tsanzirani, tsa. 63 Nsanja ya Olonda,10/1/2010, tsa. 16
21 Yehova anakomera mtima Hana moti anabereka ana ena.+ Anabereka ana aamuna atatu ndi aakazi awiri. Ndipo Samueli anapitiriza kukula akutumikira Yehova.*+