1 Samueli 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno munthu wa Mulungu anapita kwa Eli nʼkumuuza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Kodi ine sindinachititse kuti anthu amʼnyumba ya bambo ako andidziwe pamene anali akapolo kunyumba ya Farao ku Iguputo?+
27 Ndiyeno munthu wa Mulungu anapita kwa Eli nʼkumuuza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Kodi ine sindinachititse kuti anthu amʼnyumba ya bambo ako andidziwe pamene anali akapolo kunyumba ya Farao ku Iguputo?+