1 Samueli 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo mʼnyumba yanga udzangoona mdani pakati pa zinthu zonse zabwino zimene zidzachitikira Isiraeli.+ Mʼnyumba yako simudzapezekanso munthu wokalamba.
32 Ndipo mʼnyumba yanga udzangoona mdani pakati pa zinthu zonse zabwino zimene zidzachitikira Isiraeli.+ Mʼnyumba yako simudzapezekanso munthu wokalamba.