1 Samueli 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako ndidzasankha wansembe wanga wokhulupirika.+ Ameneyu adzachita mogwirizana ndi zimene mtima wanga ukufuna. Ndidzamʼmangira nyumba yokhalitsa, ndipo adzatumikira wodzozedwa wanga monga wansembe nthawi zonse.
35 Kenako ndidzasankha wansembe wanga wokhulupirika.+ Ameneyu adzachita mogwirizana ndi zimene mtima wanga ukufuna. Ndidzamʼmangira nyumba yokhalitsa, ndipo adzatumikira wodzozedwa wanga monga wansembe nthawi zonse.