1 Samueli 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa nthawi imeneyo, mwana uja Samueli ankatumikira+ Yehova moyangʼaniridwa ndi Eli. Koma mawu a Yehova anali osowa masiku amenewo ndipo anthu sankaona masomphenya+ pafupipafupi.
3 Pa nthawi imeneyo, mwana uja Samueli ankatumikira+ Yehova moyangʼaniridwa ndi Eli. Koma mawu a Yehova anali osowa masiku amenewo ndipo anthu sankaona masomphenya+ pafupipafupi.