-
1 Samueli 3:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako Yehova anabwera nʼkuima pamalopo ndipo anaitananso ngati poyamba paja kuti: “Samueli! Samueli!” Samueli anayankha kuti: “Lankhulani, ine mtumiki wanu ndikumva.”
-