-
1 Samueli 3:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ndiyeno Eli anamuuza kuti: “Kodi Mulungu wakuuza uthenga wotani? Chonde usandibisire. Mulungu akulange ndi kuwonjezerapo, ukandibisira ngakhale mawu amodzi pa mawu amene wakuuza.”
-