-
1 Samueli 3:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Choncho Samueli anamuuza zonse ndipo sanamʼbisire chilichonse. Zitatero Eli anati: “Ndi Yehova amene wanena. Achite zimene akuona kuti nʼzabwino.”
-