1 Samueli 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo Yehova anapitiriza kuonekera ku Silo, popeza Yehova anathandiza Samueli kuti amudziwe bwino. Anachita zimenezi pogwiritsa ntchito mawu a Yehova.+
21 Ndipo Yehova anapitiriza kuonekera ku Silo, popeza Yehova anathandiza Samueli kuti amudziwe bwino. Anachita zimenezi pogwiritsa ntchito mawu a Yehova.+