1 Samueli 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthuwo atabwerera kumsasa, akulu a Isiraeli ananena kuti: “Nʼchifukwa chiyani lero Yehova walola kuti Afilisiti atigonjetse?*+ Tiyeni tikatenge likasa la pangano la Yehova ku Silo+ tizikhala nalo, kuti litipulumutse mʼmanja mwa adani athu.” 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:3 Nsanja ya Olonda,9/15/2015, tsa. 27
3 Anthuwo atabwerera kumsasa, akulu a Isiraeli ananena kuti: “Nʼchifukwa chiyani lero Yehova walola kuti Afilisiti atigonjetse?*+ Tiyeni tikatenge likasa la pangano la Yehova ku Silo+ tizikhala nalo, kuti litipulumutse mʼmanja mwa adani athu.”