1 Samueli 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Apa ndiye zativuta ndithu. Ndi ndani atipulumutse mʼmanja mwa Mulungu wamkuluyu? Ameneyu ndi Mulungu amene anapha Aiguputo ambirimbiri mʼchipululu.+
8 Apa ndiye zativuta ndithu. Ndi ndani atipulumutse mʼmanja mwa Mulungu wamkuluyu? Ameneyu ndi Mulungu amene anapha Aiguputo ambirimbiri mʼchipululu.+