1 Samueli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho Afilisiti anamenyadi nkhondo ndipo Aisiraeli anagonja+ moti aliyense anathawira kutenti yake. Aisiraeli amene anaphedwa anali ambiri. Panaphedwa asilikali oyenda pansi okwana 30,000.
10 Choncho Afilisiti anamenyadi nkhondo ndipo Aisiraeli anagonja+ moti aliyense anathawira kutenti yake. Aisiraeli amene anaphedwa anali ambiri. Panaphedwa asilikali oyenda pansi okwana 30,000.