1 Samueli 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso Likasa la Mulungu linalandidwa, ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana a Eli, anaphedwa.+