1 Samueli 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsiku limenelo munthu wina wa fuko la Benjamini anathamanga kuchoka kumalo ankhondowo kukafika ku Silo, atangʼamba zovala zake ndiponso atadzithira dothi kumutu.+
12 Tsiku limenelo munthu wina wa fuko la Benjamini anathamanga kuchoka kumalo ankhondowo kukafika ku Silo, atangʼamba zovala zake ndiponso atadzithira dothi kumutu.+