1 Samueli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Afilisiti atalanda Likasa+ la Mulungu woona, analitenga ku Ebenezeri nʼkupita nalo ku Asidodi.