1 Samueli 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Atadzuka mʼmawa tsiku lotsatira, anapeza kuti Dagoni wagwanso chafufumimba patsogolo pa Likasa la Yehova. Mutu wa Dagoni ndi manja ake zinali zitaduka nʼkugwera pakhomo. Mbali yooneka ngati nsomba ndi imene inatsala.*
4 Atadzuka mʼmawa tsiku lotsatira, anapeza kuti Dagoni wagwanso chafufumimba patsogolo pa Likasa la Yehova. Mutu wa Dagoni ndi manja ake zinali zitaduka nʼkugwera pakhomo. Mbali yooneka ngati nsomba ndi imene inatsala.*