-
1 Samueli 5:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Anthu a ku Asidodi ataona zimenezi, anati: “Musalole kuti Likasa la Mulungu wa Isiraeli likhalebe kuno chifukwa iye watisautsa kwambiri pamodzi ndi mulungu wathu, Dagoni.”
-