1 Samueli 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atafika nalo kumeneko, dzanja la Yehova linakhaulitsanso anthu amumzindawo moti anasowa mtendere. Iye anachititsa kuti anthu onse a mumzindawo, kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu, adwale matenda a mudzi.+
9 Atafika nalo kumeneko, dzanja la Yehova linakhaulitsanso anthu amumzindawo moti anasowa mtendere. Iye anachititsa kuti anthu onse a mumzindawo, kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu, adwale matenda a mudzi.+