-
1 Samueli 6:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndiyeno iwo anafunsa kuti: “Kodi nsembe yakupalamula imene tiyenera kumutumizira ikhale chiyani?” Poyankha, ansembe ndi olosera aja anati: “Mutumize zifaniziro 5 zagolide za matenda a mudzi, ndi zifaniziro 5 zagolide za mbewa, mogwirizana ndi chiwerengero cha olamulira a Afilisiti.+ Muchite zimenezi chifukwa mliriwu wagwera aliyense wa inu, pamodzi ndi olamulira anu.
-