1 Samueli 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mupange zifaniziro za matenda anu a mudzi ndi zifaniziro za mbewa+ zimene zikuwononga dziko, ndipo muyenera kulemekeza Mulungu wa Isiraeli. Mukatero, mwina adzachepetsako mphamvu ya dzanja lake kwa inuyo, mulungu wanu ndi dziko lanu.+
5 Mupange zifaniziro za matenda anu a mudzi ndi zifaniziro za mbewa+ zimene zikuwononga dziko, ndipo muyenera kulemekeza Mulungu wa Isiraeli. Mukatero, mwina adzachepetsako mphamvu ya dzanja lake kwa inuyo, mulungu wanu ndi dziko lanu.+