1 Samueli 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nʼchifukwa chiyani mukuumitsa mitima yanu ngati mmene anachitira Aiguputo ndi Farao?+ Mulungu atawakhaulitsa+ analola Aisiraeli kupita ndipo iwo anapitadi.+
6 Nʼchifukwa chiyani mukuumitsa mitima yanu ngati mmene anachitira Aiguputo ndi Farao?+ Mulungu atawakhaulitsa+ analola Aisiraeli kupita ndipo iwo anapitadi.+