-
1 Samueli 6:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mupange ngolo yatsopano ndipo mutenge ngʼombe ziwiri zimene zili ndi ana, zomwe sizinanyamulepo goli, nʼkuzimangirira kungoloyo. Koma ana a ngʼombezo muwabweze kunyumba kuti asapite nawo.
-