1 Samueli 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngolo ija inafika mʼmunda wa Yoswa, wa ku Beti-semesi, ndipo inaima pafupi ndi mwala waukulu. Ndiyeno anthuwo anawaza matabwa a ngoloyo nʼkupereka ngʼombe zija+ nsembe yopsereza kwa Yehova.
14 Ngolo ija inafika mʼmunda wa Yoswa, wa ku Beti-semesi, ndipo inaima pafupi ndi mwala waukulu. Ndiyeno anthuwo anawaza matabwa a ngoloyo nʼkupereka ngʼombe zija+ nsembe yopsereza kwa Yehova.