1 Samueli 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho amuna a ku Beti-semesi ananena kuti: “Ndi ndani angaime pamaso pa Yehova Mulungu woyera+ ndipo Mulungu apita kwa ndani akatisiya?”+
20 Choncho amuna a ku Beti-semesi ananena kuti: “Ndi ndani angaime pamaso pa Yehova Mulungu woyera+ ndipo Mulungu apita kwa ndani akatisiya?”+