1 Samueli 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho amuna a ku Kiriyati-yearimu anabweradi nʼkutenga Likasa la Yehova ndipo anakaliika mʼnyumba ya Abinadabu+ imene inali paphiri. Ndiyeno anasankha* Eliezara mwana wake kuti azilondera Likasa la Yehova.
7 Choncho amuna a ku Kiriyati-yearimu anabweradi nʼkutenga Likasa la Yehova ndipo anakaliika mʼnyumba ya Abinadabu+ imene inali paphiri. Ndiyeno anasankha* Eliezara mwana wake kuti azilondera Likasa la Yehova.