1 Samueli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuchokera pamene Likasa linayamba kukhala ku Kiriyati-yearimu, panapita nthawi yaitali mpaka zinakwana zaka 20 ndipo Aisiraeli onse anayamba kufunafuna* Yehova.+
2 Kuchokera pamene Likasa linayamba kukhala ku Kiriyati-yearimu, panapita nthawi yaitali mpaka zinakwana zaka 20 ndipo Aisiraeli onse anayamba kufunafuna* Yehova.+