1 Samueli 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho iwo anasonkhana pamodzi ku Mizipa, kenako anatunga madzi nʼkuwathira pansi pamaso pa Yehova ndipo anasala kudya tsiku limenelo.+ Iwo ananena kuti: “Tachimwira Yehova.”+ Ndipo Samueli anayamba kuweruza+ Aisiraeli ku Mizipa.
6 Choncho iwo anasonkhana pamodzi ku Mizipa, kenako anatunga madzi nʼkuwathira pansi pamaso pa Yehova ndipo anasala kudya tsiku limenelo.+ Iwo ananena kuti: “Tachimwira Yehova.”+ Ndipo Samueli anayamba kuweruza+ Aisiraeli ku Mizipa.