1 Samueli 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Aisiraeli anauza Samueli kuti: “Musasiye kupemphera kwa Yehova Mulungu wathu kuti atithandize+ komanso kutipulumutsa mʼmanja mwa Afilisiti.”
8 Choncho Aisiraeli anauza Samueli kuti: “Musasiye kupemphera kwa Yehova Mulungu wathu kuti atithandize+ komanso kutipulumutsa mʼmanja mwa Afilisiti.”